Blankslate LENZ

Blankslate LENZ Professional Photography & Videography Services in Cape Town. Weddings | Events | Corporate | Content Creator |Digital Marketer

Bookings Available Nationwide.
(10)

We at Blankslate Lenz ,we treasure our clients more than anything as we know that the happiness of our clients is our sole mandate.

Akuti akufuna akafotokoze Chomwe chayambitsa ziwawa ku camp ya ku Durban komwe amalawi akukhala kutsatila ndi kuthamangi...
16/06/2026

Akuti akufuna akafotokoze Chomwe chayambitsa ziwawa ku camp ya ku Durban komwe amalawi akukhala kutsatila ndi kuthamangitsidwa Kwawo M'nyumba mwawo.

Mwatasa tu, Kuziyitanila LINDERA muli pheee,Plus Kukhala ndi criminal record m’dziko la weni...
16/06/2026

Mwatasa tu, Kuziyitanila LINDERA muli pheee,
Plus Kukhala ndi criminal record m’dziko la weni...

16/06/2026
Akuti mu July ku kubwera oyimba,Komatu oyimba amenewa, Akufuna chiyani kwa amalawi omwe ali theba???AMZAWO akuganiza zob...
16/06/2026

Akuti mu July ku kubwera oyimba,
Komatu oyimba amenewa, Akufuna chiyani kwa amalawi omwe ali theba???

AMZAWO akuganiza zobisala Iwo Ndi pamene akupanga zozawa kawa zowona??
Chabwino abwera, koma achita po chani pa za anthu akusowa chithandizo ku Durban wa???

Anthu ake tu ndi omwe wa omwe amalowa mma show awo, adakachitapo kanthu Plz...

Asamangowakonda nthawi ya Mtendere yokha, or atasonkha Ma 50 000 kwacha, ichitabe Kwakukulu than kungokhala chete...

Uwu ndi Mwayi wanu oti muphunzire chi Afrikaans....Maiwatu adapita Kwa baby dad Yemwe contract idatha kale, kukayitanits...
16/06/2026

Uwu ndi Mwayi wanu oti muphunzire chi Afrikaans....

Maiwatu adapita Kwa baby dad Yemwe contract idatha kale, kukayitanitsa ndalama ya chithandizo cha mwana fodya Ali m'manja paja yao ija ma kek...

Ndiyetu kudali kulalata panja Pa mpanda Wa baby dad wo...
Mix mai wa ndi osaloledwa Kuti azipezeka chifupi Ndi bamboyo.

Mai wa ndi ozunguza Ndiye bambo adapita ku khothi kukatenga Protection Order....
Video ili ku comment section ko..

Chatulukira cha komaliza pamene 30 JUNE wayandikira...Koma mzimai uyuyu Eehhh...Akuti ndi mzika Ya Theba....
16/06/2026

Chatulukira cha komaliza pamene 30 JUNE wayandikira...
Koma mzimai uyuyu Eehhh...
Akuti ndi mzika Ya Theba....

Ndiye kwatulukiranso Mzimai wina Ku Johannesburg ku Primrose uyu Ndiye Ndiye eehh  ayi zikomo...Mu ma film ama NIGERIA m...
16/06/2026

Ndiye kwatulukiranso Mzimai wina Ku Johannesburg ku Primrose uyu Ndiye Ndiye eehh ayi zikomo...
Mu ma film ama NIGERIA muja amafunika MO sure...
Lero pano akupanga ma demo ndi gulu lake ku Primrose ko...
Khalani osamalitsa abale amene mumakhala Kumeneko...

Ma demo ku SEA POINT ayambika, koma utati uone Mwa cheka utha kumaona Ngati akupanga chitelera...Anthu ake ndi 8...Video...
16/06/2026

Ma demo ku SEA POINT ayambika, koma utati uone Mwa cheka utha kumaona Ngati akupanga chitelera...
Anthu ake ndi 8...
Video ili ku comment section ko

SIZIKUMVETSETSEKA OR NDI PANG’ONO.Boma lathu lidakayamba layimitsa kaye Kuti Anthu Ku theba asamapite kukagwira ntchito ...
16/06/2026

SIZIKUMVETSETSEKA OR NDI PANG’ONO.

Boma lathu lidakayamba layimitsa kaye Kuti Anthu Ku theba asamapite kukagwira ntchito kwa chaka chino.

Zinthu pa theba pano sizili bwino koma daily anthu akulowa be.

Bola likudzatuta Anthu othawa ziwawa Ku theba kuno ndi ma bus 10,
Pomwe daily almost ma bus 4 kapena 6 akutuluka mmalawi ndi kumabwera Ku theba.

Zimenezo sizikupanga sense or Ndi pang’ono...

Anthu omwe akubwera theba wa, adzangofikila mmavuto ndi kumafunanso thandizo la boma,
Bwanji nanga bomalo osachita po kanthu before it's too late...

Anthu ku theba kuno akuvutika.
Ma guys ku malawi ko dziwani zimenezo...

PLZ imitsani Ma program anu obwera theba wo kaye...

Theba wawola uyu..
Apolice ayamba kuyenda door to door,
Zinthu zaima nawonso ma landlord akukana Ndalama Ya rent akuopa kugumulidwa Ma nyumba awo.
Mabwana nawo akuopa kulipira chindaputsa Cha 100 thousand Rand.

Ndiye wina kumabwera be....
Kaya...

Address

227 Mainroad
Cape Town
7800

Opening Hours

Monday 07:00 - 19:00
Tuesday 09:00 - 19:00
Wednesday 09:00 - 19:00
Thursday 09:00 - 19:00
Friday 09:00 - 19:00
Saturday 09:00 - 19:00
Sunday 09:00 - 19:00

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Blankslate LENZ posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Blankslate LENZ:

Share