23/12/2021
uja wayankhula ekha k*t akungoyenera kuvomeleza nyengo mmene iliri ππππ
Tikunena pano wamuika eli njuchi pa show yake ya ku L city k*t akapange perfom
Inu mutipo chani?? sangie wapanga zolondora kapena ayi??
moti lero sangie wamusankha eli k*t akhare ngat model πππ mu nyimbo yake kuchokera mu abulm yake yomwe yatuluka posachedwayi ndipo nyimboyi ikujambulidwa ku mzuzu lero ndipo after kujambula kwa lero tiponya ka clip/short video ka nyimboyi pa page yomwey k*t mufire
Pangan follow page yi potobwanya profile pic yo ndikupanga click botton la k*t kasakuphonyeni
Thanksππππππππ