17/02/2026
Madzulo a lero lachiwiri (Tuesday) pa 17 february 2026 tiyamba kuwufunafuna mwezi wa ramadhan in Sha Allah, ndipo ngati uwoneke ndiye kuti mmawa lachitatu pa 18 February ndi 1 Ramadhan koma ngati siwuwoneka ndiye kuti timaliza chiwelengelo cha Shabana 30 days ndipo tizayamba kusala pa 19 february in sha Allah..
Uthenga ukabwera wakuoneka mwezi in sha Allah will let you know.
Remember anthu ena ku Malawi calendar ya Shaban ndi 28 izi zikutanthauza kuti iwowo lero sangasake nawo mwezi..pomwe ife calendar ya ummul-qura ikuti 29
Choncho alemekezeni omwe akusalira pachisankho chawo....
Chaka chino tiyeni tipewe zokangana,tipange practice ibada imeneyi mopanda kutozana zala ,mwina Allah angayike mmitima mwathu ikhlas.
Ramadhan mubarak!!