Msash

Call Directions Website Contact the business

Msash Wedding Photographer
Video Director
Entrepreneur
Content Creator
for business, contact
📥 [email protected]

Ona nzeru,,,Photographed by Msash
23/10/2026

Ona nzeru,,,
Photographed by Msash

22/10/2026

Ngakhale kutentha kufike 60°C, ife tisambabe madzi otentha! 😂🥵💦♨️🌡️🤒

Madzi ozizira Ayi!!!! tinapangidwa mosiyana! 🤣🔥😂

Ma set a clean.. Happy birthday Constance Photographed by: Msash
21/10/2026

Ma set a clean.. Happy birthday Constance
Photographed by: Msash

17/10/2026

KUPHUNZIRA PHOTOGRAPHY & VIDEOGRAPHY — LESSON 7 (in chichewa)

LEAVE SPACE (NEGATIVE SPACE) — KUSIYA MALO PA CHITHUNZI

🤣😂 Kodi umajambula munthu n’kumudzaza pa chithunzi chonse ngati kuti palibe malo ena? Eeh, photographer iwe! 😂📸

Lero tikuphunzira njira imodzi yofunika kwambiri pa Composition yotchedwa Leave Space (Negative Space).

15/10/2026

KUPHUNZIRA PHOTOGRAPHY & VIDEOGRAPHY — LESSON 6 (in chichewa): RULE OF THIRDS

Ukamajambula munthu umangomuika pakati pa chithunzi nthawi zonse? Eeh, photographer iwe!

Lero tikuphunzira njira imodzi yokonzera zinthu pa chithunzi kuti chizioneka chokongola komanso cha professional!

Funso: Kodi umakonda kuika munthu pakati kapena kumbali ya chithunzi?
Follow Msash for more updates

15/10/2026

Happy mother's day to all mothers
Anyadireni Amayi anu mu comment section

14/10/2026

KUPHUNZIRA PHOTOGRAPHY NDI VIDEOGRAPHY — LESSON #5: COMPOSITION

Tsopano ndi nthawi yanu yosankha!

Ndi njira iti ya Composition yomwe mukufuna kuti ndiyambe kuphunzitsa?

1️⃣ Rule of Thirds – Kugawa chithunzi m’magawo atatu kuti zinthu zikhale pamalo oyenera.

2️⃣ Leading Lines – Kugwiritsa ntchito mizere kuti itsogolere maso a munthu amene akuona chithunzi kapena vidiyo.

3️⃣ Negative Space (Leave Space) – Kusiya malo opanda zinthu zambiri m’chithunzi kuti chinthu chachikulu chiwonekere bwino.

Kumbukirani: Kujambula zithunzi kapena mavidiyo abwino sikudalira kamera yomwe mumagwiritsa ntchito yokha, komanso mmene mumakonzekeretsera ndi kuyikamo zinthu m’chithunzi chanu!

Mu phunziroli, tiyamba kuphunzira za Composition mmene tingakonzekeretsere zinthu m’chithunzi kapena vidiyo kuti zioneke zokongola, zogwirizana komanso zopereka uthenga womveka bwino.

Lembani nambala ya njira yomwe mukufuna kuti ndiyambe nayo mu COMMENT!
Follow Msash for more updates

13/10/2026

GOAL PREDICTION TIME
Zimbabwe’s Mighty Warriors Vs Malawi’s Scorchers
TWO LUCKY” winners will get 5pin each. Let’s go

Ma Set a clean, Happy birthday little ShazirahPhotographed by Msash
13/10/2026

Ma Set a clean, Happy birthday little Shazirah
Photographed by Msash

Happy birthday Beatrice Photographed by Msash
13/10/2026

Happy birthday Beatrice
Photographed by Msash

Address

Area 21
Lilongwe

Opening Hours

Monday 09:00 - 19:30
Tuesday 09:00 - 19:30
Wednesday 09:00 - 19:30
Thursday 09:00 - 19:30
Friday 09:00 - 19:30
Saturday 09:00 - 19:30
Sunday 09:00 - 19:30

Telephone

+265881996090

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Msash posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Msash:

Shortcuts

Share