Ministry of Worship/intercession

Ministry of Worship/intercession the page is about god news.

29/09/2025

Kupephela kumafunika kulimba

09/10/2024

Osataya yesu kamba ka mavuto,mulungu amafuna moyo uzikhala mkochokela.

17/05/2024

mulungu akutisunga ndi zolinga,tikamasauka akufuna moyowu ukhale ndi mbili,chofunika osasiya kumulambila.ambuye akudalitseni

22/12/2023

Tiyeni tipephere mosalakeza pamene
Yesu ukubadwa

14/11/2023

Kwamene mukutsatila minstry of worship/intercession,posachedwapa tikhala tikugawana mawuthenga abwino komaso ma vidioz chondee auwuzeni azanu ambiri.

Thawi iyi imakhala yokhudza pomwe tikudya thupi la ambuye yesu,pomwe tikhala tikusathula mitima yathu pazomwe takhla tik...
25/09/2023

Thawi iyi imakhala yokhudza pomwe tikudya thupi la ambuye yesu,pomwe tikhala tikusathula mitima yathu pazomwe takhla tikuchita,pakuti mawu amati muzichita ichi kuti muzinikumbukila ambuye akudalitseni pomwe mulandila mkatewu ndi kumwera chikho cha mwazi wambuye wathu yesu khristu amen!!.

25/09/2023

Yesu mwini adati ine ndi njila ndi chowonadi palibe adza kwa atate kopanda one,mawuwa amawuza yani?ndipo amatatahauzanji?

18/08/2023

Kugawana uthenga wa ambuye sikulakwa,ukamva mawu tizichita changu ndi kutembenuka mtima.

21/07/2023

Tiyeni tisamalire miyoyo yathuyi mulungu azikudalitsani amene mukutsatira gulu lino zikomo.

Address

KU
Lilongwe

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Ministry of Worship/intercession posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Ministry of Worship/intercession:

Share

Category