21/10/2026
ππ₯ FUNSO LA LERO! ππ
Tiyeni ticheze kaye! π€£π
Ngati pali chinthu chimodzi chimene simungafune kuti chidzakubweretseni mavuto pa moyo wanu, chingakhale chiyani? ππ
π Ngongole?
π€£ Ma ex?
π Mabwenzi achinyengo?
π Chikondi chosapita bwino?
π Kapena zinthu zina zomwe tikudziwa tokha? π€£π€£
Lembani yankho lanu mu comment! ππ₯π
Musaope kunena zoona, pano tikungosangalala! π€£π Koma osatchula mayina a anthu, tisayambitse nkhondo! πππ₯
The Promix World Hub πβ€οΈβπ₯
ππ₯