29/04/2026
"Angadzaone Ngati Moyo Ndiophweka"
M***a "The Boika" Mkwanda wati nthawi yakwana k*ti Roy Yudah Afunde lona. "ndikumufuna ndikamugonekeko pansi angawone ngati moyo ndiwophweka", Mkwanda wayankhula.
Awa ndi machine nokhaso mungathe kuona.
Source Malawi Boxing News