Mudzi wathu mobile photo studio

Mudzi wathu mobile photo studio Helping students reaching out their goes regardless weather they're coming from rich or poor families

02/09/2022

Ife amudzi wathu cholinga chathu mkuthandiza kupitisa pasogolo maphuzilo muno mmalawi maka popanga ma I D photos kwaulere Kwa ana ovutikisisa

01/09/2022

Uthenga wapadera

Tikukudziwitsani kuti tatsekula organisation komwe kakutchedwa kuti mudzi wathu mobile photo studio.

Kwathawi yaitali ana omwe akulemba mayeso mdziko mwathu muno akhala akukumana ndimavuto ambili lina mwa ILO ndi kusapeza ndalama zojambulitsira ma ID awo pomwe akuyandikila kulemba mayeso. Izi zilichoncho chifukwa chakuti makolo ambili ndiovutikila mmapezedwe azachuma.

2. Kulephera kuiika information yolondola pamalo oyenera kutero maka kubungwe lolembetsa mayeso MANEB kumapangisaso kuti ana ambili asalembenawo mayeso.Izi zilichoncho chifukwa chakuti pamafunikaso ndalama zina zokakozesera vutoli ndipo ndalamazo amaperekaso ndimakolo koma ngati sanakakozetse ndiyekuti ophuzilayo salembanawo mayesowa. Ndipo zimalimbikisaso kuti tizibwererabe mmbuyo mmalo mopita patsogolo.

Nde ineyo ndaazanga ngati amalawi okhudzidwa tinachionakuti mchapamwamba kuti tithandizane/ tigwire tchit ndaaphuzitsi kuti tichepese mavuto amenewa. Ndiye ka organisation kathuka ndikoti tizijambula ana ndikuwapangila ma ID photo pompo pompo in 2 seconds mmapulaiyamale ndiso mmasekondale sukulu.

Tikatere ndekuti tithandiza kupitisa patsogolo maphunziro mdziko lathu lino chifukwa palibe ophuzila or ndimmodzi adzanene kuti sindinalembe mayeso chifukwa chavuto la ID ayi,

Note: Ka organisation Ka sikofuna kupeza phindu komabe ana azidzapephedwa kulipira kandalama kochepa mcholinga choti tizikwanisa kugulira zipangizo kuti tithandizirekoso ena, koma kwa okhawo ovutikisisa tizathandiza mpaka alembe mayeso awo popanda chovuta chilichose

Mchifkwa chni mukuyenera sukulu yanu ikuyenera kukhala membala wathu?
1. Ndife otchipa chifukwa tikuthandiza mtundu waamalaw
2.Timabwera mkujambula pathawi yomwe mwatitana
3. Ngti pakapzeka mistake ina kubugwe lolembetsa mayeso MANEB ife timabwra mkukujambulirani ana Anu ulere
4.ndife odalilika chifukwa timalolaso ngati muli membala wathu kukujambulirani pakapita thawi mudzatipasa timalipiroto.

Gawan uthngawu kumaglu ose makas kwaphzts ±27736844037

01/09/2022

Special announcement to everyone
Hy ladies and gents

We have opened the small organisation that aims to provide crucial services in our community schools. Ever since our school candidates has been starving when it comes to write their examination especially PLSCE, JCE and MSCE. This is so, just because every candidate is asked to have ID , so our candidates especially in villages they're always at a risk because some of them, 1. their parents cannot afford it in time 2. Systematic errors, this happens when the examination board try to put every candidate's info on their IDs they sometimes missplace (instead of putting the name of the owner of the I'd they do visa es) when this happens it needs a teacher to find his/her own money to go correct it or otherwise that student will never write the examination. So me and my colleagues as a concerned citizens we are to start working with teachers in order to eliminate this situation, so that no candidate will complain that he/she didn't write her examination just because she didn't pay ID fee in time or their was an error which was not sorted out in time. For more information. +27736844037 what's app. U will speak to Mr stonard

Address

Lilongwe
Lilongwe

Opening Hours

Monday 09:00 - 17:00
Tuesday 09:00 - 17:00
Wednesday 09:00 - 17:00
Thursday 09:00 - 17:00
Friday 09:00 - 17:00
Saturday 09:00 - 17:00
Sunday 09:00 - 17:00

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Mudzi wathu mobile photo studio posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category