Noise Malawi

Noise Malawi Professional Live Stream Producer & Photographer
Helping churches, events & weddings go live in excellence. SlingLight_Photography

06/10/2026

3mins

Malawi 0 vs 1 Algeria

03/10/2026

TOMBSTONE UNVEILING INVITATION

In Memory of:

Goodwell Sapala
Batson Sapala
Elifa Sapala

Nkhani ya chisoni 💔💔😭Anthu anayi afa kutsatira ngozi ya pamsewu yomwe yachitika dzulo mu msewu wapakati pa Mchinji ndi L...
28/08/2026

Nkhani ya chisoni 💔💔😭

Anthu anayi afa kutsatira ngozi ya pamsewu yomwe yachitika dzulo mu msewu wapakati pa Mchinji ndi Lilongwe (M12), m'mudzi mwa Kankhande m'boma la Mchinji.

Mneneri wa polisi ya Mchinji a Limbani Mpinganjira atsimikiza za nkhaniyi ponena kuti ngoziyi inakhudza thiraki ya mtundu wa Volvo , NE 7828, komanso njinga ya moto ya mtundu wa Lifani yopanda nambala.

Malingana ndi a Mpinganjira, galimotoyo inaphulika tayala lakutsogolo zomwe zinapangitsa kuti dalayivala wake,a Peter Kadozo azaka 47, akanike kuyiwongolera bwino.

Izi ati zinachititsa kuti galimotoyo ikawombe njinga ya moto ya Lifani yomwe imabwera kutsogolo kwake ikuyendetsedwa ndi nzika ya dziko la Zambia, a Charles Petro azaka 29, omwenso ananyamula mayi wina a Lainess Davite azaka 23 omwe anali ndi mwana wa zaka zitatu.

Kutsatira ngoziyi, anthu onse omwe anakwera njinga yamotoyo komanso a Francis Mwafongo azaka 42 omwe anali mu galimotoyo anavulala kwambiri m'mutu ndipo anatsimikizika kuti amwalira atawatengera ku chipatala cha boma la Mchinji.

  An unidentified driver is suspected to have sustained injuries after the vehicle they were driving was involved in a r...
28/08/2026




An unidentified driver is suspected to have sustained injuries after the vehicle they were driving was involved in a road accident in Blantyre.

The accident occurred near the Blantyre Water Board offices, around the former Blantyre Dairy Board premises.

According to observations at the scene, the vehicle was travelling from Kamuzu Stadium towards Ndirande when it reportedly veered off the road and hit a concrete street light pole.

The circumstances that led to the accident remain unclear.

The extent of the driver's injuries has also not yet been established, while further details are expected as authorities continue with investigations.

Tiwa ndi mayi afuko...
27/08/2026

Tiwa ndi mayi afuko...

Tiwa savage wati ayiimba nyimbo ndi modzi mwawoimba nyimbo muno Malawi Temwa
27/08/2026

Tiwa savage wati ayiimba nyimbo ndi modzi mwawoimba nyimbo muno Malawi Temwa

Happy birthday suffix
27/08/2026

Happy birthday suffix

  Jetu atulusa nyimbo Lero
27/08/2026



Jetu atulusa nyimbo Lero

   arrests two NOCMA officials over USD403,615 fraud incident
26/08/2026



arrests two NOCMA officials over USD403,615 fraud incident

 Akatswiri a mdziko la China aulutsa tindege (drones) toyatsa nyali mlengalenga tokwana 500  ngati mbali imodzi ya mwamb...
21/08/2026



Akatswiri a mdziko la China aulutsa tindege (drones) toyatsa nyali mlengalenga tokwana 500 ngati mbali imodzi ya mwambo wokondwerera zaka 77 zakukhazikitsidwa kwa dzikolo.

Mwambowu wachitikira mu mzinda wa Lilongwe.

Kudzera mu tindegeti, akatswiriwa aonetsa chifanizo cha nkhope ya mtsogoleri wa dziko lino a Peter Mutharika, osewera a timu ya dziko lino ya Scorchers ndi ntchito zosiyanasiyana zimene dzikolo lachita mdziko muno.

Address

Blantyre

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Noise Malawi posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share